Malawi Music

Prince Chitz Watulusa Vidiyo Yatsopano Yakuti Meka

Download Prince Chitz Watulusa Vidiyo Yatsopano Yakuti Meka

Katswili wolemba ndi woimba nyimbo wa ku Malawi Prince Chitz watulusa vidiyo ya nyimbo yomwe anajambula yakuti Meka. 

Meka ndi nyimbo yokoma yokamba pa chikondi, vidiyo yake yaikometselako moti sitikukaikila kuti muikonda nanunso. Chifukwa chake ni chakuti woimbayu, ali ndi luso lakuimba ndipo vidiyo iyi ndi yokondweletsanso. 

Iyi nyimbo, ikamba pa m’mene munthu ayenela kukondela wokondedwa wake. Ndipo sitikukaikila kuti nyimbo iyi ikazikavinidwa kuma mwambo wa ukwati

Zokondweletsanso ni zakuti, Prince Chitz akuimba mokoma moti fans ya ku Zambia ikukondwela naye ndipo akufuna zina. Uyu ni ulendo wa woimbayu, ndipo mu chaka cha 2024, tikuyembekezela zambili kuchokela kwa iye.

Chotsangalatsa ni chakuti, munga tambe vidiyo iyi pamene pano pa Zedbusy.com munsimu. Ioneleleni.

Related Articles

Back to top button