VideosZambian Music Muchi Nyanja

Kondwa – Unisiye Vidiyo Ya Mau

Download Kondwa – Unisiye Vidiyo Ya Mau

Kondwa, Mkazi woimba wamuzambia watulusa vidiyo ya mau ya nyimbo yake yakuti ‘Unisiye’ yomwe anachotsa posachedwa apa.

Unisiye nikanyimbo kamushe kamene ka kamba pali zachikondi, koma mwachisoni, chikondi chimene chisila.

Komanso iphunzitsa kuti, ngati munthu wasiya kumukonda, ni bwino kumuuza kuti azibe ndipo aoneko ena amene angamukonde mosataya nthawi. Mau amene ali munyimbo iyi ni ogwira mutima. Pamene mukuinvelela muza njoya kwambili chifukwa cha mwanene iyendela.

Kondwa wankhala akutulusa ma nyimbo ya bwino, ya tanthauzo komanso yoimbidwa bwino monga “Mwaibala“. Izi zimachitika chifukwa cha voice yake komanso kalembedwe kake.

Tambani vidiyo iyi pansi apa. Tiziwa kuti muzakondwela nayo.

Onaninso: Don Kingston ft. Dismanto – Hule Vidiyo

Phiri

As a Zambian music enthusiast with a passion for writing and extensive industry knowledge, I can help your music get the attention it deserves. With captivating and compelling write-ups, I’ll ensure your sound resonates with fans worldwide. Contact us today to make your music heard!.

Related Articles

Back to top button