Malawi Music

Dj Kachamba ft. General Kanene – Miseche Mp3

Download Dj Kachamba ft. General Kanene – Miseche Mp3

Dj Kachamba wapha nnyimbo inanso yotchedwa Miseche ndi General Kanene waku Zambia. 

Nyimboyi ndi yophunzitsa kenakake ndi m’mene timakhalila ndi anthu ena. Kamba ka ukhalidwe wabwino, sibwino kuma nenezana. Iyi ndi ndemanga za Dj Kachamba ndi General Kanene mu nyimbo yakuti Miseche.

Chonde, Mvetselani Miseche pansipa ndi kuchita Daunilodi komanso kuonelera pa YouTube vidiyo ya mapikicha.

Onaninso: Towela Kaira ft. Bloodkid Yvok, Majoos & Xaven – Zingati Video

Related Articles

Back to top button